Bengo aba nthuli Bengo mu ndege Social network Mai Bengo Bengo ndi abusa ake “Tiye tikametetse ulele”“Ndi omwe akukumetaniwotu”

BENGO NDI MKAZI WAKE

Mai Bengo: bola akanandikwatira Satanatu. Mwina akanandisamala.

Bengo: Mukanangomangidwatu chabe chifukwa malamulo a dziko lino amaletsa kukwatirana pa chibale.

Mai Bengo: Mmmmm ?




Back Home Up